24/11/2025
Tili pa Google Maps tsopano! 📍🔥
Pano palibe kusochela—Chillaz Bar ili pa map.
Mukangolemba “Chillaz Bar”, Google imangoti “Tiyeni!” 😆
Tikukupemphani kuti mutipatse ma rating ndi review pogwiritsa ntchito link iyi:
👉https://g.page/r/CTkWJreT9Hy1ECA/review
Zikomo kwambiri.
Mubwere kudya vibe… osati kungodutsa! 🍻😂
Post a review to our profile on Google