ARISE FOODS

ARISE FOODS We offer Lunch and supper, we also deliver!enjoy the hotel standard food!We also Carter for weddings, church events, birthday and any other events!

Good news !!!! Good news !!!! Good news Kuli mwayi oti m***a kuphunzila ma business ang'ono ang'ono pa mtengo wa ziiii,N...
25/08/2025

Good news !!!! Good news !!!! Good news

Kuli mwayi oti m***a kuphunzila ma business ang'ono ang'ono pa mtengo wa ziiii,Ndi k15,000 yokha m***a kuphunzira luso la ntchito za manja zosiyana siyana,Timaphunzitsa kapangidwe ka sausage,cake,ma doughnuts komanso ndi zina zambiri.Anthu Inu Kodi simufuna kuziyimira panokha?Inu kupempha kumatukwanitsa πŸ˜ƒπŸ˜ƒπŸ˜ƒπŸ˜ƒ,komanso akutali sinawayiwaleyi pa phone p***a ndimaphunzitsanso ndithu mpamtengonso wa ziiiii ,Pamapeto pa zonse ndimapeleka pamphlet ya ma recipe omwe ndaphunzitsa komanso ma recipe ena 15 owonjezera ,komanso pamakhala competition yopanga bake pakutha pa class Ina iliyonse,opambana amalandila mphoto zosiyana siyanaπŸ₯³πŸ₯³πŸ₯³ ,mukafuna kudziwa zambiri ndiyankhuleni pa number iyi

WhatsApp: 0992672858

*Learn, Bake, and Succeed! πŸŽ‚*

"

"Rise to the Occasion with Arise Bakery! πŸ°πŸ‘©β€πŸ³Join our baking classes and learn the art of baking from experienced instru...
27/07/2025

"Rise to the Occasion with Arise Bakery! πŸ°πŸ‘©β€πŸ³

Join our baking classes and learn the art of baking from experienced instructors!

*Online Baking Course:* MK 5,000 (learn from the comfort of your home)
*Face-to-Face Training:* MK 15,000 (hands-on experience, limited space)
*Individual Lessons:* Customized packages available (prices vary depending on duration)

At Arise Bakery, we're passionate about helping you develop your baking skills. Join us and become a baking pro! πŸŽ‰

Contact us to register or learn more: [0992672858 or join our Whatsapp group
https://chat.whatsapp.com/BXsbIQ8YagqIYaeXB2Wo1B?mode=ac_t] for more information...

25/05/2025

Its an Exciting NewsπŸ’ƒπŸ½πŸ’ƒπŸ½πŸ’ƒπŸ½πŸ’ƒπŸ½

*"Sweet Success Awaits! πŸŽ‰πŸ°*

Join *ARISE Online Baking Class* and unlock your baking potential! πŸžοΈπŸ‘¨β€πŸ³

*Learn from the comfort of your home* with our expert guidance and step-by-step instructions.

*What's in it for you?*

✨ Master the art of baking delicious treats
✨ Gain confidence in the kitchen
✨ Learn new recipes and techniques
✨ Connect with fellow baking enthusiasts

*Investment:* MK5,000 (an investment in your sweet success!)

*Class Starts:* 31st May 2025!

*The Sweetest Competition! πŸ°πŸ†*

After classes, showcase your baking skills! The student who bakes the most impressive treat will receive an award:

*MK20,000 Cash Prize! πŸ’Έ*

*Ready to rise to the occasion?* Join ARISE Online Baking Class and start baking your way to success! πŸŽ‚

*Register Now!* Call or WhatsApp +265 992672858 to secure your spot! πŸ“²

*Limited spots available!* Don't miss out on this sweet opportunity! 🍰"

30/01/2025

Welcome to Arise Online Baking Course

Kuli mwayi ophunzira kuphika ndi ku baker Online koma mtengo wa ziii...Anthu akuphunzira online kutenga ma certificate, diploma, degree e.t.c Nanga Inu mungalephere kuphunzira kuphika through phone ndikusintha moyo wanu nkuyamba business yanu...kupempha kumatukwanitsa anthuni...

Ili ndi group lomwe timaphunzitsa China chilichonse chokhuza Baking...

Course Outline

*What is Baking
*Types of Baking
*Baking Materials
*Measurements
*Types of cake Flour and their use
*Differents between baking powder and Baking soda
*Common Baking Mistakes
*Different types of cakes
*Ways of baking soft,moist and fluffy cakes
*How to make a Bread
*Butter cookies
*Wedding Cakes
*Cake Decorations
*Cake drippings
*What you need when baking
*Types of baking pans and sizes
*How to attract more customers
*Presentation of your items
*Pizza
*Milk scones

Follow this link to join my WhatsApp group:

*ARISE BAKERY*Pali mwayi ophunzira kuphika komanso kupanga bake...Ife a ARISE timaphunzitsa kuzera pa phone komanso face...
30/10/2024

*ARISE BAKERY*

Pali mwayi ophunzira kuphika komanso kupanga bake...Ife a ARISE timaphunzitsa kuzera pa phone komanso face to face..

Mukafuna kukhala Amodzi awophunzira pa phone(Online), Lembesani ndi k2500 yokha basi ndipo muphunzira zonsezi zili munsimu😊😊, ma classes azayamba pa 01 November Friday ---- 03 November Sunday 2024.Pamene Mzuzu training izakhalako pa 16 November.

1. Banana Cake
2. Cookies
3. Potato Salad
4. Tomato Puree
5. Classic Beef Stew
6. Potato Crisps
7. Lettuce Salad
8. Meat Pie
9. Chicken/beef Stir fry
10. Zebra cake
11. Samoosa
12. Chapatti
13. Chocolate cake
14. Watermelon Juice
15. Zitumbuwa
16. Coslaw Salad

WhatsApp on 0992672858 for more information

Kwa amene akufuna kuphunzira nawo ,ya online, training ndi mawa pa 24 May  at only k5,000 ,muzaphunzira kapangidwe ka sa...
23/05/2024

Kwa amene akufuna kuphunzira nawo ,ya online, training ndi mawa pa 24 May at only k5,000 ,muzaphunzira kapangidwe ka sausage,cake,doughnuts ndi samosa.Komanso kwa amene akufuna kuphunzira face to face ndipa 1 june 2024.kuzakhala kuphunzira macake,sausage,samosa ndi ma doughnuts pa mtengo wa k10,000.pamapeto pake muzalandila machine opangira sausage.komanso kuzanyamula zomwe mwapanga.

Ndimatenga anthu 20 okha.Amene apange register nsanga machine awo akhalanso ready nsanga.
Registration fee ndi k800.training fee imapelekedwa tsiku lozaphunzira
Whatsapp me on 0992672858 for more

Opportunity
11/05/2024

Opportunity

08/05/2024
K4000....0884166355/0998821815
05/04/2024

K4000....0884166355/0998821815

At Kande Serving Foccapso Mzuzu Chapter...
15/10/2023

At Kande Serving Foccapso Mzuzu Chapter...

Address

Katoto
Mzuzu

Opening Hours

Monday 07:30 - 00:00
Tuesday 07:30 - 00:00
Wednesday 07:30 - 00:00
Thursday 07:30 - 00:00
Friday 07:30 - 00:00
Saturday 07:30 - 00:00
Sunday 12:00 - 00:00

Telephone

+265884166355

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when ARISE FOODS posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Restaurant

Send a message to ARISE FOODS:

Featured

Share

Category