Innobuild Limited Company

Innobuild Limited Company Land Development, Construction, Maintenance on Credit, Architectural Designs
(1)

02/10/2026

Hoozah friday Innobuilders
Lilongwe Chiuzira ndi Njewa site's ngati mwakonzeka Go konko

Mukafuna kumva zambiri
0991148500/0888002899

30/09/2026

Area 23 Chiuzira Site Launch
09991148500 and 0888002899

Going Live Chiuzira Area 23 Lilongwe Site Launch
30/09/2026

Going Live Chiuzira Area 23 Lilongwe Site Launch

Your Host Fumbanani Chirambo A.K.A the Land Doc Fumbanani Will be LIVE at 2:30 masanawa lero tikuti LeroZisakuphonyeni  ...
30/09/2026

Your Host Fumbanani Chirambo A.K.A the Land Doc Fumbanani
Will be LIVE at 2:30 masanawa lero tikuti Lero
Zisakuphonyeni

Mukudziwa kale tikupanga za Area 23 Chiuzira site 🔥 kwachemeratu uku...

pachiongolero
0991148500/0888002899

Big Happy birthday to Mr KalimbaDecades with the team is no small achievement - it's huge! Thanks for your Loyalty,Hard ...
29/09/2026

Big Happy birthday to Mr Kalimba

Decades with the team is no small achievement - it's huge! Thanks for your Loyalty,Hard work and for always bringing humor to the team.

May God add more years, more blessings and more wins 🙏

Get set for the next post kukubwera bomba

28/09/2026

Mongo kumbutsana chabe
Lilongwe Area 23 Chiuzira site kwayaka 🔥

Cash ndi 1,950,000 yokha basi

Kulipira kwa chaka chimodzi 2,500,000 kuyamba ndi 500,000 yokha basi

Komaso kulipira kwa Zaka Two ndi 3,000,000
Kuyamba ndi 650,000 yokha basi

Size 15 by 30m per plot

Nanga tingalime
0991148500/0888002899

Land Development, Construction, Maintenance on Credit, Architectural Designs

28/09/2026

Ayi sakukamenya munthu a land doctorwa
Koma akukaonetsa ku Area 23 Chiuzira site 🔥
Yomwe yayaka moto ku Lilongwe

Kumeneko cash price ndi 1,950,000
12 months payment 2,500,000
24 months payment 3,000,000
Standard plot size 15 by 30m

Pangani machawi mitengo imeneyi ili valid mpaka pa 15th Oct 2026
0991148500/0888002899

25/09/2026

Aja mumafuna ma plots ku 23 Chiuzila just 600mtrs from chiuzira filling station tiyeni uku, very fast developing site, only 45 plots available, kulipila for 24 months.

Ukuku ndi first come first serve, osadikira athe call 0991 14 85 00 /0888002899

This is only from Innobuild Limited Company

#

Akulu akulu amati zabwino Sizichedwa kuzepulidwaChitani machawi kuti ulendo uno mukhale MtikaMukafuna kumva zambiri 0991...
24/09/2026

Akulu akulu amati zabwino Sizichedwa kuzepulidwa
Chitani machawi kuti ulendo uno mukhale Mtika

Mukafuna kumva zambiri
0991148500/0888002899

Wamwayi ndi wamwayi ma tickets nde alipo  Pangani video mukuyimba nyimbo ya Alex Nkalo iliyonse ndikupanga tag Innobuild...
23/09/2026

Wamwayi ndi wamwayi ma tickets nde alipo

Pangani video mukuyimba nyimbo ya
Alex Nkalo iliyonse ndikupanga tag
Innobuild Limited Company komaso Alex Nkalo

Komaso osaiwala kuwawuza aneba kuti malo olipira momverera akupezeka ku Innobuild konkha (12 to 24 months payment plan)
Call or Whatsapp on
0991148500/0888002899

Address

P. O. BOX 1967 LILONGWE
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Innobuild Limited Company posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share