Ghetto chilling zone

Ghetto chilling zone Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Ghetto chilling zone, Bar & Grill, . com, Zomba.

25/08/2022

*MWANA SALAKWA
*
TEACHER : Mada

Mada : Yes madamu!

TEACHER : ukadzakula umafuna udzakhale ndani?

Mada : mkufuna nzakhale ozembetsa mankhwala ozunguza bongo, nzapita nawo ku Dubai kenako kuChina, nzapha aliyense onditsata, nzamanga nyumba za pamwamba ku Canada, Northern Ireland komanso ku Paris. Nzakwatira mwachangu mzamugulira mkazi wanga ndege yake yake. Ngati angandipemphe 1 million kwacha nzamupasa, 10 million kwacha.

TEACHER : Will you shut up! Stupid boy! Sit down my friend, sukudziwa chimene ukuyankhula. Tamala, stand up uyiwudze kalasi ukadzakula umafuna udzakhale ndani.

Tamala: nzakhala mkazi wa Mada

@* _Ambassador🇲🇼_

27/07/2022
05/07/2022

M'NYAMATA WA ZAKA 19 ADAGWILILIRA MSUNGWANA WA ZAKA 16 - PACHIFUKWACHI ZAKA 7 KUNDENDE

M'nyamata wina wa zaka 19 m'boma la Mwanza wagamulidwa kukakhala ku ndende kwa zaka 7 chifukwa chogwililira msungwana wa zaka 16.

CPM News yapeza kuti m'nyamatayi dzina lake ndi Charles Walasi Christopher ndipo adapalana ubwenzi ndi msungwanayi kuyambila m'mwezi wa May.

Kenako Charles wapeleka mimba kwa msungwanayi ndipo makolo a msungwanayi atadziwa kuti wawo wayima, adakatula Nkhaniyi ku Polisi ndipo Charles wapezeka olakwa pa mlandu ogwililira.

-Mirriam Butao



Address

@MKbrighton. Com
Zomba

Telephone

+265888327488

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ghetto chilling zone posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Featured

Share

Category