Notafa Enterprises 1

  • Home
  • Notafa Enterprises 1

Notafa Enterprises 1 Agri inputs, extension services,fruit production and supplier( the biggest papaya farm in Malawi)

Soon in our shop at Notafa
21/09/2026

Soon in our shop at Notafa

Pamene mwadzala mbewu izi,tomatoes,eggplants or therere ndipo mukuwopa kangaude ( red spider mites).Ngati mulibe abamect...
05/09/2026

Pamene mwadzala mbewu izi,tomatoes,eggplants or therere ndipo mukuwopa kangaude ( red spider mites).Ngati mulibe abamectin m***a kugwilitsa ntchito profenofos ngati Snowcron.Nthawi inoyo nde pachimake pa kangaude.

Zikomo

One mistake famous do is mixing amamectine+ Mancozeb in one tank.The effectiveness of amamectine is drastically reduced....
01/09/2026

One mistake famous do is mixing amamectine+ Mancozeb in one tank.The effectiveness of amamectine is drastically reduced.Combination ya chabe.

Vitamin D reduced dementia by 40%, Reduced - "Carcasses Strewn" (Majesty From Within 2018 | New Standard Elite), Colles' Fracture Reduction Trainer, Flo Rida - Low (feat. T-Pain) [from Step Up 2 The Streets O.S.T. / Mail On Sunday] (Official Video)

Wow.....we are still pushing
01/09/2026

Wow.....we are still pushing

Mukamapopera Tomato, nthawi zina mudzisintha sprayer nozzle position.Pena  idzithila itayang'ana kumwamba kuti ithile ku...
25/08/2026

Mukamapopera Tomato, nthawi zina mudzisintha sprayer nozzle position.Pena idzithila itayang'ana kumwamba kuti ithile kunsi kwa masamba.Pali mankhwala ena omwe ndi a contact basi,zilombo zikabisala ukuku Zina zimatha kupulumuka.Komanso booster amalowa bwino from the underside of a leaf.

24/08/2026

Please Tomato amafunika Potassium and Phosphorus ochuluka.Ngati muli ndikuthekera kadzithilani Super D compound or D compound.Kwinako mudzingopopela foliar oti mulinso calcium.

Ku Malawi kuno mitundu ya feteleza oyenera ndi yosowa kwambili.....nzosiyana ndiku Zambia.

A single step....
21/08/2026

A single step....

17/08/2026

Mbewu.Mankhwala.Ulangizi wa ulere.....

Ntcheu boma
Close to Masa or Mtsitsa building chaku nsika

Timafika ku munda kwanu,kukupatsani uphungu mwa ulere

Terms and conditions apply.

17/08/2026

Rainy season fungicide program Tomatoes (Kukonzekera)

Week 1 (Day 1):
Metalaxyl + Mancozeb (e.g Romaxil,Succes,Metalyx etcl) – Provides strong systemic and curative deep-tissue clean up ngati matenda ayamba kuwoneka.

Week 2 (Day 7):

Mancozeb 80% WP or Daconil– Kuthana ndi njere zonse zoyambitsa chiwawu mmasamba.

Week 3 (Day 14):

Cymoxanil + Mancozeb (e.g., Curzate or Victory) –
Pena achina Folicur( Tebunocozole) Kuthana ndi njere pa masamba,kuchiza plus kuteteza

Week 4 (Day 21):

Copper-based fungicide (e.g., Copper Oxychloride)
Kutetezaku bacterial spots komanso chiwawa.

Visit us in Ntcheu ( kwa shop ya M'tsitsa kunsika) for comprehensive programs on various crops

Address

P. O Box 158, Senzani

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Notafa Enterprises 1 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

  • Want your restaurant to be the top-listed restaurant?

Share