12/09/2026
Good Morning Family and Friends
Apapa Ana akutsegulira ma school
Ndekuti ma order a zakudya tizipanga weekend yokhayokha.
Tsabola ekha nde azipezeka even nkati mwa week co, amakhala opangidwa kale.
Mwamugulira kale bag ina mwanayo kapena mwangosintha zip?๐๐๐๐