30/09/2023
Next week ndikupita kumudzi ndikatsazikane ndi big....Dedza is Mourning, malawi is too...
Thupi la malemu a John Zenus Ungapake Tembo aliyika m'manda lachitatu sabata ya mmawa pa 4 October 2023, m'mudzi mwa Kaphala TA Kaphuka Ku Dedza.
Lolemba pa 2 October 2023,Thupi la malemuwa akalitenga Ku nyumba ya chisoni Ku Goodwill kupita nalo Ku ofesi za chipani cha MCP komwe kukakhale mwambo oona nkhope ndipo madzulo apita nalo ku nyumba yawo Ku area 10 ku Lilongwe komweko.
Lachiwiri pa 3 October 2023,thupili azalitengera pa Malawi Square Ku BICC komwe kukakhale mwambo wa mapemphero kenaka azapita nalo ku mudzi kwawo ku Dedza.
(by Chikondi Mphande-Dedza:9/29/2023)